Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 29:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo uzilandire m'manja mwao, ndi kuzipsereza pa guwa la nsembe, pa nsembe yopsereza, zicite pfungo lokoma pamaso pa Yehova; ndiyo nsembe yamoto ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:25 nkhani