Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 29:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo uiphe nkhosa yamphongoyo, nutapeko pa mwazi wace, ndi kuupaka pa ndewerere ya khutu lamanja la Aroni, ndi pa ndewerere ya khutu lamanja la ana ace amuna, ndi pa cala cacikulu ca dzanja lao lamanja, ndi pa cala cacikulu ca phazi lao lamanja, ndi kuuwaza mwaziwo pa guwa la nsembe posungulira,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:20 nkhani