Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mpango wa efodi, wokhala pamenepo, kuti ammange nao, ukhale wa ciombedwe comweco, ndi woombera kumodzi, wagolidi, ndi thonje lamadzi, ndi lofiirira ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:8 nkhani