Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo azibvale Aroni, ndi ana ace, pakulowa iwo ku cihema cokomanako, kapena poyandikiza iwo ku guwa la nsembe kutumikira m'malo opatulika; anganyamule mphulupulu, nangafe; likhale lemba losatha la iye ndi mbumba zace pambuyo pace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:43 nkhani