Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zobvala azisoka ndizi: capacifuwa ndi efodi, ndi mwinjiro, ndi malaya opikapika, ndi nduwira, ndi mpango; tero apangire Aroni mbale wako ndi ana ace zobvala zopatulika, kuti andicitire Ine nchito ya nsembe,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:4 nkhani