Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Upangenso mphete ziwiri zagolidi, ndi kuzimanga pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'munsi, ku mbali yace ya kutsogolo, pafupi pa msoko wace, pamwamba pa mpango wa efodi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:27 nkhani