Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma nsonga zace ziwiri za maunyolo opotawo uzimange ku zoikamo ziwiri, ndi kuziika pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'tsogolo mwace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:25 nkhani