Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo akuyandikire Aroni mbale wako, ndi ana ace amuna pamodzi naye, mwa ana a Israyeli, kuti andicitire Ine nchito ya nsembe, ndiwo Aroni, Nadabu, ndi Abihu, Eleazara ndi ltamara, ana a Aroni.

2. Ndipo usokere Aroni mbale wako zobvala zopatulika, zikhale zaulemerero ndi zokoma.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28