Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 27:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipanga zotayira zace zakulandira mapulusa ace, ndi zoolera zace, ndi mbale zowazira zace, ndi mitungo yace, ndi zoparira moto zace; zipangizo zace zonse uzipanga zamkuwa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 27

Onani Eksodo 27:3 nkhani