Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 27:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemonso pa mbali ya kumpoto m'utali mwace pakhale nsaru zocingira za mikono zana limodzi m'utali mwace; ndi nsici zace makumi awiri, ndi makamwa ao akhale amkuwa; zokowera za nsicizo ndi mitanda yace zikhale zasiliva.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 27

Onani Eksodo 27:11 nkhani