Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzicinga nsaru yocinga pa zokowerazo, nulowetse likasa la mboni kukati kwa nsaru yocinga; ndipo nsaru yocingayo idzakugawirani pakati pa malo opatulika ndi malo opatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:33 nkhani