Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakhale matabwa asanu ndi atatu, ndi makamwa ao asiliva, ndiwo makamwa khumi mphambu asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:25 nkhani