Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 25:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipanga coikapo nyali ca golidi woona; coikapoco cisulidwe mapangidwe ace, tsinde lace ow thupi lace; zikho zace, mitu yace, ndi maluwa ace zikhale zocokera m'mwemo;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 25

Onani Eksodo 25:31 nkhani