Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 24:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Ndipo maonekedwe a ulemerero wa Yehova anali ngati mota wonyeketsa pamwamba pa phiri, pamaso pa ana a Israyeli.

18. Ndipo Mose analowa m'kati mwa mtambo, nakwera m'phirimo; ndipo Mose anakhala m'phiri masiku makumi anai usana ndi usiku.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 24