Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 23:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalemba malire ako kuyambira ku Nyanja Yofiira, kufikira ku nyanja ya Afilisiti, ndi kuyambira kucipululu kufikira ku Nyanja; popeza ndidzapereka okhala m'dzikolo m'dzanja lako, ndipo uziwaingitsa pamaso pako.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 23

Onani Eksodo 23:31 nkhani