Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 23:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uzibweca nazo zoyambayamba za m'munda mwako ku nyumba ya Yehova Mulungu wako. Usaphike mwana wa mbuzi mu mkaka wa mace.Mulungu aloniezana nao za Kanani.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 23

Onani Eksodo 23:19 nkhani