Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 23:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uzisunga madyerero a mkate wopanda cotupitsa; masiku asanu ndi awiri uzidya mkate wopanda cotupitsa, monga ndinakuuza, nyengo yoikika, mwezi wa Abibu, pakuti m'menemo unaturuka m'Aigupto; koma asaoneke munthu pamaso panga opanda kanthu;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 23

Onani Eksodo 23:15 nkhani