Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 22:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mlandu uti wonse wa colakwa, kunena za ng'ombe, za buru, za nkhosa, za cobvala, za kanthu kali konse kotayika, munthu anenako kali kace; mlandu wa onse awiri ufike kwa oweruza; iye amene oweruza amtsutsa alipe cowirikiza kwa mnansi wace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 22

Onani Eksodo 22:9 nkhani