Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 21:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ngati ng'ombe ikatunga masiku adapitawo, ndipo anamcenjeza mwiniyo, koma osaisunga iye, ndipo ikapha mwamuna kapena mkazi, aiponye miyala ng'ombeyo, ndi mwini waceyo amuphenso.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:29 nkhani