Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 20:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Undiumbire guwa la nsembe ladothi, nundiphere pomweponsembe zako zopsereza, ndi nsembe zako zamtendere, nkhosa zako ndi ng'ombe zako; pali ponse ndikumbukiritsa anthu dzina langa ndidzakudzera ndi kukudalitsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 20

Onani Eksodo 20:24 nkhani