Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 20:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usasirire nyumba yace ya mnzako, usasirire mkazi wace wa mnzako, kapena wanchito wace wamwamuna, kapena wanchito wace wamkazi, kapena ng'ombe yace, kapena buru wace, kapena kanthu kali konse ka mnzako.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 20

Onani Eksodo 20:17 nkhani