Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma tsiku lacisanu ndi ciwiri ndilo Sabata la Yehova Mulungu wako; usagwire nchito iri yonse, kapena iwe wekha, kapena mwana wako wamwamuna, kapena mwana wako wamkazi, kapena wanchito wako wamwamuna, kapena wanchito wako wamkazi, kapena nyama zako, kapena mlendo amene ali m'mudzi mwako;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 20

Onani Eksodo 20:10 nkhani