Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anati, Wakuika iwe ndani ukhale mkuru ndi woweruza wathu? kuteroku ukuti undiphe, monga unamupha M-aigupto? Ndipo Mose anacita mantha, nanena, Ndithu cinthuci cadziwika.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 2

Onani Eksodo 2:14 nkhani