Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, ngati mudzamvera mau anga ndithu, ndi kusunga cipangano canga, ndidzakuyesani cuma canga ca padera koposa mitundu yonse ya anthu; pakuti dziko lonse lapansi ndi langa;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:5 nkhani