Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anakwera kwa Mulungu; ndipo Yehova ali m'phirimo anamuitana, ndi kuti, Uzitero kwa mbumba ya Yakobo, nunene kwa ana a Israyeli, kuti,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:3 nkhani