Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo phiri la Sinai linafuka monsemo, popeza Yehova anatsikira m'moto pamenepo; ndi utsi wace unakwera ngati utsi wa m'ng'anjo, ndi phiri lonse linagwedezeka kwambiri,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:18 nkhani