Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali tsiku lacitatu, m'mawa, panali mabingu ndi zimphezi, ndi mtambo wakuda bii paphiripo, ndi liu la lipenga lolimbatu; ndi anthu onse okhala kutsasa ananjenjemera.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:16 nkhani