Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 18:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akakhala nao mlandu adza kwa ine, kuti ndiweruze pakati pa munthu ndi mnansi wace, ndi kuti ndiwadziwitsemalemba a Mulungu, ndi malamulo ace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 18

Onani Eksodo 18:16 nkhani