Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 18:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yetero, wansembe wa Midyani, mpongozi wa Mose, anamva zonse zimene Mulungu adacitira Mose ndi Israyeli anthu ace, kuti Yehova adaturutsa Israyeli m'Aigupto.

2. Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ace awiri;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 18