Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 17:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacha dzina la malowo Masa, ndi Meriba, cifukwa ca kutsutsana kwa ana a Israyeli; popezanso anayesa Yehova, ndi kuti, Kodi Yehova ali pakati pa ife, kapena iai?

Werengani mutu wathunthu Eksodo 17

Onani Eksodo 17:7 nkhani