Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena nao, Ici ndi comwe Yehova analankhula, Mawa ndiko kupuma, Sabata lopatulika la Yehova; cimene muzioca, ocani, ndi cimene muziphika phikani; ndi cotsala cikukhalireni cosunguka kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 16

Onani Eksodo 16:23 nkhani