Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena ndi anthu, Musaope, cirimikani, ndipo penyani cipulumutso ca Yehova, cimene adzakucitirani lero; pakuti Aaigupto mwawaona lerowa simudzawaonansokonse.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:13 nkhani