Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 13:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Ndipo Yehova anawatsogolera usana ndi mtambo njo kuwatsogolera m'njira; ndi usiku ndi moto njo, wakuwawalitsira; kuti ayende usana ndi usiku;

22. sanacotsa mtambo usana, kapena mtambo wamoto usiku, pamaso pa anthu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13