Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 13:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunakhala pamene Farao adalola anthu amuke, Mulungu sanawatsogolera njira ya dziko la Afilisti, ndiyo yaifupi; pakuti Mulungu anati. Angadodome anthuwo pakuona nkhondo ndi kubwerera m'mbuyo kumka ku Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13

Onani Eksodo 13:17 nkhani