Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 12:49-51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

49. Pakhale lamulo lomweli pa wobadwa m'dziko, ndi pa mlendo wakukhala pakati pa inu.

50. Ndipo ana onse a Israyeli anacita monga Yehova adawalamulira Mose ndi Aroni, momwemo anacita.

51. Ndipo kunakhala tsiku lomwelo, kuti Yehova anaturutsa ana a Israyeli m'dziko la Aigupto, monga mwa makamu ao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 12