Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muzitenga mpukutu wa hisope, ndi kuubviika m'mwazi uli m'mbale, ndi kupaka mwazi uli m'mbalemo pa mphuthu ya pamwamba ndi pambali; koma inu, asaturuke munthu pakhomo pa nyumba yace kufikira m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 12

Onani Eksodo 12:22 nkhani