Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lino lidzakhala kwa inu cikumbutso, muzilisunga la madyerero a Yehova; ku mibadwo yanu muzilisunga la madyerero, likhale lemba losatha.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 12

Onani Eksodo 12:14 nkhani