Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 10:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo lidzakuta nkhope ya dziko, kotero, kuti palibe munthu adzakhoza kuona dziko; ndipo lidzadya zotsalira zidapulumuka, zidatsalira inu pamatalala, ndipo lidzadya mtengo uti wonse wokuphukirani kuthengo;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:5 nkhani