Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ndi Aroni analowa kwa Farao nanena naye, Atero Yehova, Mulungu wa Ahebri, Ukana kudzicepetsa pamaso panga kufikira liti? Lola anthu anga amuke, akanditumikire;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:3 nkhani