Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anaitana Mose, nati, Mukani, tumikirani Yehova; nkhosa zanu ndi ng'ombe zanu zokha zitsale; mumuke nao ana anu ang'ononso.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 10

Onani Eksodo 10:24 nkhani