Koma iwo ndiwo anthu anu ndi colowa canu, amene mudaturutsa ndi mphamvu yanu yaikuru ndi dzanja lanu lotambasuka.