Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 9:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Yehova anakutumizani kucokera ku Kadesi Barinea, ndi kuti, Kwerani, landirani dziko limene ndakupatsani; munapikisana nao mau a Yehova Mulungu wanu, osamkhulupirira, kapena kumvera mau ace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:23 nkhani