Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinatenga cimo lanu, mwana wa ng'ombe mudampangayo, ndi kumtentha ndi moto, ndi kumphwanya, ndi kumpera bwino kufikira atasalala ngati pfumbi; ndipo ndinataya pfumbi lace m'mtsinje wotsika m'phirimo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:21 nkhani