Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinagwa pansi pamaso pa Yehova, monga poyamba paja, masiku makumi anai usana ndi usiku, osadya mkate osamwa madzi, cifukwa ca macimo anu onse mudacimwa, ndi kucita coipaco pamaso pa Yehova, kuutsa mkwiyo wace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:18 nkhani