Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 9:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinatembenuka ndi kutsika m'phiri, ndi phirilo linatentha ndi moto; ndi magome awiri a cipangano anali m'manja mwanga.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:15 nkhani