Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Imvani Israyeli; mulikuoloka Yordano lero lino, kulowa ndi kulandira amitundu akuru ndi amphamvu akuposa inu, midzi yaikuru ndi ya malinga ofikira kuthambo,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 9

Onani Deuteronomo 9:1 nkhani