Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 8:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga amitundu amene Yehova awaononga pamaso panu, momwemo mudzaonongeka; cifukwa ca kusamvera mau a Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8

Onani Deuteronomo 8:20 nkhani