Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wanu adzataya amitundu awa pang'ono pang'ono; simuyenera kuwaononga msanga, kuti zingakucurukireni zirombo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:22 nkhani