Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anapatsa zizindikilo ndi zozizwa zazikuru ndi zowawa m'Aigupto, pa Farao, ndi pa nyumba yace yonse, pamaso pathu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:22 nkhani