Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 5:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muziyenda m'njira yonse imene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani, kuti mukakhale ndi moyo, ndi kuti cikukomereni, ndi kuti masiku anu acuruke m'dziko limene mudzakhala nalo lanu lanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5

Onani Deuteronomo 5:33 nkhani